Numeri 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Tsopano atsogoleri a masauzande a asilikali+ anafika kwa Mose. Iwowa anali atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100.+
48 Tsopano atsogoleri a masauzande a asilikali+ anafika kwa Mose. Iwowa anali atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100.+