-
Numeri 31:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Golide yense amene anam’pereka kwa Yehova anakwana masekeli 16,750. Uyu ndiye golide amene anaperekedwa ndi atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100.
-