Numeri 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ife sitidzalandira nawo cholowa tsidya ilo la Yorodano kupita kutsogoloko, chifukwa cholowa chathu chili tsidya lino la Yorodano, kum’mawa kuno.”+
19 Ife sitidzalandira nawo cholowa tsidya ilo la Yorodano kupita kutsogoloko, chifukwa cholowa chathu chili tsidya lino la Yorodano, kum’mawa kuno.”+