Numeri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 mpaka dzikolo litagonjetsedwa pamaso pa Yehova.+ Pambuyo pake mudzabwerere.+ Ngati muchitadi zimenezi, mudzakhala opanda mlandu kwa Yehova ndi kwa Isiraeli. Ndipo dzikoli lidzakhaladi lanu, monga cholowa chanu pamaso pa Yehova.+
22 mpaka dzikolo litagonjetsedwa pamaso pa Yehova.+ Pambuyo pake mudzabwerere.+ Ngati muchitadi zimenezi, mudzakhala opanda mlandu kwa Yehova ndi kwa Isiraeli. Ndipo dzikoli lidzakhaladi lanu, monga cholowa chanu pamaso pa Yehova.+