Numeri 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako ana a Makiri+ mwana wa Manase, ananyamuka ulendo wopita kumzinda wa Giliyadi. Analanda mzindawo ndi kupitikitsa Aamori amene anali kukhalamo.
39 Kenako ana a Makiri+ mwana wa Manase, ananyamuka ulendo wopita kumzinda wa Giliyadi. Analanda mzindawo ndi kupitikitsa Aamori amene anali kukhalamo.