-
Numeri 35:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Komanso musalandire dipo loperekedwa ndi cholinga chofuna kuwombola munthu amene anathawira kumzinda wothawirako kuti abwerere kwawo mkulu wa ansembe asanamwalire.
-