Deuteronomo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 âNdiyeno tinatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana. Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nafe nkhondo ku Edirei.+
3 âNdiyeno tinatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana. Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nafe nkhondo ku Edirei.+