Deuteronomo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake. Umuchite zimene unachitira Sihoni+ mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.’
2 Chotero Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake. Umuchite zimene unachitira Sihoni+ mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.’