Deuteronomo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri+ ndi a Amaakati,+ ndipo midzi ya ku Basana imeneyo anaitcha dzina la iye mwini lakuti, Havoti-yairi*+ kufikira lero.
14 “Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri+ ndi a Amaakati,+ ndipo midzi ya ku Basana imeneyo anaitcha dzina la iye mwini lakuti, Havoti-yairi*+ kufikira lero.