Deuteronomo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Usadzipangire fano+ kapena chifaniziro+ cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cha m’madzi a pansi pa dziko lapansi.*
8 “‘Usadzipangire fano+ kapena chifaniziro+ cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cha m’madzi a pansi pa dziko lapansi.*