Deuteronomo 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Motero Yehova anamva mawu anu onse amene munalankhula nane, ndipo Yehova anapitiriza kundiuza kuti, ‘Ndamva mawu amene anthu awa akuuza. Mawu onse amene akuuza ali bwino.+
28 “Motero Yehova anamva mawu anu onse amene munalankhula nane, ndipo Yehova anapitiriza kundiuza kuti, ‘Ndamva mawu amene anthu awa akuuza. Mawu onse amene akuuza ali bwino.+