Deuteronomo 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse,+ chifukwatu mtundu wanu unali waung’ono mwa mitundu yonse.+
7 “Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse,+ chifukwatu mtundu wanu unali waung’ono mwa mitundu yonse.+