Deuteronomo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Pa nthawi imeneyo Yehova anandiuza kuti, ‘Dzisemere miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija,+ ndipo udzipangire likasa lamatabwa.+ Ukatero ukwere m’phiri muno kwa ine.
10 “Pa nthawi imeneyo Yehova anandiuza kuti, ‘Dzisemere miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija,+ ndipo udzipangire likasa lamatabwa.+ Ukatero ukwere m’phiri muno kwa ine.