Deuteronomo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:12 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 25 Nsanja ya Olonda,10/1/2009, tsa. 10
12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+