Deuteronomo 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti masiku anu ndi masiku a ana anu achuluke+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo anu kuti adzawapatsa,+ kuti masikuwo achuluke monga masiku a thambo lokhala pamwamba pa dziko.+
21 kuti masiku anu ndi masiku a ana anu achuluke+ m’dziko limene Yehova analumbirira makolo anu kuti adzawapatsa,+ kuti masikuwo achuluke monga masiku a thambo lokhala pamwamba pa dziko.+