Deuteronomo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Motero muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu, mwa kusunga malamulo ake+ onse amene ndikukupatsani lero, kuti muzichita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+
18 Motero muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu, mwa kusunga malamulo ake+ onse amene ndikukupatsani lero, kuti muzichita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+