Deuteronomo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:21 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 279/15/2004, tsa. 26
21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+