Deuteronomo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uzikumbukira kuti unali kapolo ku Iguputo,+ ndipo uzisunga ndi kutsatira malamulo amenewa.+