Deuteronomo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ukapeza munthu wakufa pathengo, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako, ndipo amene wapha munthuyo sakudziwika,+
21 “Ukapeza munthu wakufa pathengo, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako, ndipo amene wapha munthuyo sakudziwika,+