Deuteronomo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo akulu a mzindawo azitenga ng’ombeyo ndi kutsikira nayo kuchigwa* chokhala ndi madzi ndithu, chigwa chimene sichinalimidwepo kapena kubzalidwa mbewu. Akafika kumeneko aziipha mwa kuithyola khosi.+
4 Pamenepo akulu a mzindawo azitenga ng’ombeyo ndi kutsikira nayo kuchigwa* chokhala ndi madzi ndithu, chigwa chimene sichinalimidwepo kapena kubzalidwa mbewu. Akafika kumeneko aziipha mwa kuithyola khosi.+