Deuteronomo 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Usavale chovala chimene anachiwomba mophatikiza ubweya wa nkhosa ndi ulusi wa thonje.+