17 Pano akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi+ kuti: “Ndaona kuti palibe umboni wosonyeza kuti mwana wanuyu anali namwali.”+ Koma nawu umboni wa unamwali wa mwana wanga.’ Pamenepo azifunyulula chofunda pamaso pa akulu a mzinda.