Deuteronomo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uzikapita kwa wansembe+ amene azidzatumikira masiku amenewo ndi kumuuza kuti, ‘Ndikuvomereza lero pamaso pa Yehova Mulungu wako, kuti ndalowadi m’dziko limene Yehova analumbirira makolo athu kuti adzatipatsa.’+
3 Uzikapita kwa wansembe+ amene azidzatumikira masiku amenewo ndi kumuuza kuti, ‘Ndikuvomereza lero pamaso pa Yehova Mulungu wako, kuti ndalowadi m’dziko limene Yehova analumbirira makolo athu kuti adzatipatsa.’+