Deuteronomo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo tinayamba kufuulira Yehova Mulungu wa makolo athu,+ ndipo Yehova anamva mawu athu+ ndi kuona nsautso yathu, mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu.+
7 Pamenepo tinayamba kufuulira Yehova Mulungu wa makolo athu,+ ndipo Yehova anamva mawu athu+ ndi kuona nsautso yathu, mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu.+