Deuteronomo 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yang’anani pansi kuchokera kumwamba, kumalo anu oyera okhalako,+ ndipo mudalitse anthu anu Aisiraeli+ ndi dziko limene mwatipatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene munalumbirira makolo athu.’+
15 Yang’anani pansi kuchokera kumwamba, kumalo anu oyera okhalako,+ ndipo mudalitse anthu anu Aisiraeli+ ndi dziko limene mwatipatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene munalumbirira makolo athu.’+