Deuteronomo 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+
16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+