Deuteronomo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usapatuke pa mawu onse amene ndikukulamula lero, kupita kudzanja lamanja kapena lamanzere+ kuti utsatire milungu ina ndi kuitumikira.+
14 Usapatuke pa mawu onse amene ndikukulamula lero, kupita kudzanja lamanja kapena lamanzere+ kuti utsatire milungu ina ndi kuitumikira.+