Deuteronomo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+
43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+