Deuteronomo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako+ kuti uwatsatire.+
14 Pakuti mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako+ kuti uwatsatire.+