Deuteronomo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:12 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 39/15/2004, tsa. 273/15/2000, tsa. 17
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi.