Yoswa 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ili ndilo dziko limene ana a Gadi+ anapatsidwa monga cholowa chawo potsata mabanja awo. Anapatsidwa mizinda ya kumeneko ndi midzi yake yomwe.
28 Ili ndilo dziko limene ana a Gadi+ anapatsidwa monga cholowa chawo potsata mabanja awo. Anapatsidwa mizinda ya kumeneko ndi midzi yake yomwe.