Yoswa 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malire a kumadzulo anali Nyanja Yaikulu+ ndi gombe lake. Amenewa ndiwo anali malire onse a ana a Yuda potsata mabanja awo.
12 Malire a kumadzulo anali Nyanja Yaikulu+ ndi gombe lake. Amenewa ndiwo anali malire onse a ana a Yuda potsata mabanja awo.