Yoswa 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malirewo anakhotera kumadzulo n’kubwerera ku Azinotu-tabori, n’kupitirira mpaka kukafika ku Hukoku ndi ku Zebuloni+ kum’mwera. Anakafikanso ku Aseri+ kumadzulo, ndi kotulukira dzuwa ku Yuda,+ kumtsinje wa Yorodano.
34 Malirewo anakhotera kumadzulo n’kubwerera ku Azinotu-tabori, n’kupitirira mpaka kukafika ku Hukoku ndi ku Zebuloni+ kum’mwera. Anakafikanso ku Aseri+ kumadzulo, ndi kotulukira dzuwa ku Yuda,+ kumtsinje wa Yorodano.