Oweruza 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngelo wa Yehova atalankhula mawu amenewa kwa ana onse a Isiraeli, anthuwo anayamba kulira mokweza mawu.+
4 Mngelo wa Yehova atalankhula mawu amenewa kwa ana onse a Isiraeli, anthuwo anayamba kulira mokweza mawu.+