-
Oweruza 6:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndipo umangire Yehova Mulungu wako guwa lansembe mwa kuyala miyala. Ulimange pamwamba pa linga la malo otetezekawa. Ukatero, utenge ng’ombe yaing’ono yamphongo yachiwiri ija, ndi kuipereka monga nsembe yotentha ndi moto pankhuni za mzati wopatulika umene udulewo.”
-