-
Oweruza 7:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako anawauza kuti: “Muonetsetse ndi kuphunzira pa zimene ine ndikuchita, ndipo nanunso muchite zomwezo. Ndikakafika m’malire a msasa, zimene ine ndikachite, nanunso mukachite zomwezo.
-