Oweruza 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “N’chifukwa chake Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m’manja mwanga, ndithu, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga ya m’chipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+
7 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “N’chifukwa chake Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m’manja mwanga, ndithu, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga ya m’chipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+