Oweruza 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anapitiriza ulendo wake kuchoka kumeneko n’kupita ku Penueli.+ Atafika ku Penueli, anawapemphanso chimodzimodzi, koma amuna a kumeneko anamuyankha mofanana ndi mmene amuna a ku Sukoti anamuyankhira.
8 Choncho anapitiriza ulendo wake kuchoka kumeneko n’kupita ku Penueli.+ Atafika ku Penueli, anawapemphanso chimodzimodzi, koma amuna a kumeneko anamuyankha mofanana ndi mmene amuna a ku Sukoti anamuyankhira.