Oweruza 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zeba ndi Zalimuna atathawa, iye mosazengereza anawathamangitsa mpaka kuwagwira mafumu a Midiyaniwa.+ Atatero, anachititsa gulu lawo lonse kunjenjemera ndi mantha.
12 Zeba ndi Zalimuna atathawa, iye mosazengereza anawathamangitsa mpaka kuwagwira mafumu a Midiyaniwa.+ Atatero, anachititsa gulu lawo lonse kunjenjemera ndi mantha.