Oweruza 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho, Gidiyoni anapita kwa amuna a mumzinda wa Sukoti ndi kuwauza kuti: “Kodi Zeba ndi Zalimuna si awa? Aja amene munandinyoza nawo ponena kuti, ‘Tipatsirenji anyamata ako otopawo mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?’”+
15 Choncho, Gidiyoni anapita kwa amuna a mumzinda wa Sukoti ndi kuwauza kuti: “Kodi Zeba ndi Zalimuna si awa? Aja amene munandinyoza nawo ponena kuti, ‘Tipatsirenji anyamata ako otopawo mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?’”+