Oweruza 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Gidiyoni anafunsa Zeba ndi Zalimuna+ kuti: “Kodi amuna amene munapha ku Tabori+ anali otani?” Poyankha iwo anati: “Iwo anali ngati iweyo. Maonekedwe ake aliyense wa iwo anali ngati mwana wa mfumu.”
18 Tsopano Gidiyoni anafunsa Zeba ndi Zalimuna+ kuti: “Kodi amuna amene munapha ku Tabori+ anali otani?” Poyankha iwo anati: “Iwo anali ngati iweyo. Maonekedwe ake aliyense wa iwo anali ngati mwana wa mfumu.”