Oweruza 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 m’kachisi wa Baala-beriti+ ndi kum’patsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa ntchito ndi achipongwe+ kuti azim’tsatira.
4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 m’kachisi wa Baala-beriti+ ndi kum’patsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa ntchito ndi achipongwe+ kuti azim’tsatira.