Oweruza 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mtengo wa maoliviwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kutulutsa mafuta amene amagwiritsidwa ntchito potamanda+ Mulungu ndi anthu, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+
9 Koma mtengo wa maoliviwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kutulutsa mafuta amene amagwiritsidwa ntchito potamanda+ Mulungu ndi anthu, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+