Oweruza 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poyankha mtengo wa mpesawo unati, ‘Kodi ndisiye vinyo wanga watsopano amene amasangalatsa Mulungu ndi anthu,+ n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’
13 Poyankha mtengo wa mpesawo unati, ‘Kodi ndisiye vinyo wanga watsopano amene amasangalatsa Mulungu ndi anthu,+ n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’