Oweruza 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Tsopano kodi mwachita zimenezi m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, moti mwalonga Abimeleki ufumu?+ Ndipo kodi Yerubaala ndi nyumba yake mwamuchitira zinthu zabwino? Kodi mwamuchitira mogwirizana ndi zimene iye anachita,
16 “Tsopano kodi mwachita zimenezi m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, moti mwalonga Abimeleki ufumu?+ Ndipo kodi Yerubaala ndi nyumba yake mwamuchitira zinthu zabwino? Kodi mwamuchitira mogwirizana ndi zimene iye anachita,