Oweruza 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi inu mwaukira nyumba ya bambo anga lero kuti muphe ana ake+ aamuna 70+ pamwala umodzi, kuti muike Abimeleki, mwana wa kapolo wake wamkazi,+ kukhala mfumu+ yolamulira nzika za Sekemu chifukwa chakuti ndi m’bale wanu?
18 Kodi inu mwaukira nyumba ya bambo anga lero kuti muphe ana ake+ aamuna 70+ pamwala umodzi, kuti muike Abimeleki, mwana wa kapolo wake wamkazi,+ kukhala mfumu+ yolamulira nzika za Sekemu chifukwa chakuti ndi m’bale wanu?