Oweruza 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati lero mwachitira zimenezi Yerubaala ndi a m’nyumba yake m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, sangalalani ndi Abimeleki ndipo nayenso asangalale nanu.+
19 Ngati lero mwachitira zimenezi Yerubaala ndi a m’nyumba yake m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, sangalalani ndi Abimeleki ndipo nayenso asangalale nanu.+