Oweruza 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Patapita nthawi, Gaala+ mwana wa Ebedi anatuluka ndi kuima pachipata cha mzinda. Ndiyeno Abimeleki ndi anthu amene anali naye anadzuka m’malo amene anam’bisalira.
35 Patapita nthawi, Gaala+ mwana wa Ebedi anatuluka ndi kuima pachipata cha mzinda. Ndiyeno Abimeleki ndi anthu amene anali naye anadzuka m’malo amene anam’bisalira.