Oweruza 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Gaala ataona anthuwo, nthawi yomweyo anauza Zebuli kuti: “Taona, anthu akutsika kuchokera pamwamba pa mapiri.” Koma Zebuli anati: “Si anthu amenewo, ukuona zithunzithunzi za mapiri.”+
36 Gaala ataona anthuwo, nthawi yomweyo anauza Zebuli kuti: “Taona, anthu akutsika kuchokera pamwamba pa mapiri.” Koma Zebuli anati: “Si anthu amenewo, ukuona zithunzithunzi za mapiri.”+