-
Oweruza 9:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Zitatero Abimeleki anakwera phiri la Zalimoni+ pamodzi ndi anthu onse amene anali naye. Tsopano Abimeleki anatenga nkhwangwa m’manja mwake, n’kudula nthambi ya mtengo, ndipo nthambiyo anainyamula n’kuiika paphewa lake. Pamenepo anauza anthu amene anali naye kuti: “Zimene mwaona ine ndikuchita, muchitenso zomwezo mofulumira!”+
-